Yesaya 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+Amamutenga nʼkukamuika pamalo ake ndipo mulunguyo amangoima pomwepo. Sasuntha pamene amuikapo.+ Anthuwo amamuitana mofuula, koma sayankha.Sangapulumutse munthu amene ali pamavuto.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:7 Yesaya 2, tsa. 99
7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+Amamutenga nʼkukamuika pamalo ake ndipo mulunguyo amangoima pomwepo. Sasuntha pamene amuikapo.+ Anthuwo amamuitana mofuula, koma sayankha.Sangapulumutse munthu amene ali pamavuto.+