Yesaya 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kumbukirani zinthu zoyambirira zimene zinachitika kalekale,Kuti ine ndine Mulungu ndipo palibenso wina. Ine ndine Mulungu ndipo palibe aliyense wofanana ndi ine.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:9 Yesaya 2, tsa. 100
9 Kumbukirani zinthu zoyambirira zimene zinachitika kalekale,Kuti ine ndine Mulungu ndipo palibenso wina. Ine ndine Mulungu ndipo palibe aliyense wofanana ndi ine.+