Yesaya 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndikuitana mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa,*+Ndikuitana munthu kuchokera kudziko lakutali kuti adzachite zolinga zanga.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita. Ndakonza kuti zimenezi zichitike komanso ndidzazichita.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2024, tsa. 30 Yesaya 2, ptsa. 102-103 Nsanja ya Olonda,8/15/1999, tsa. 14 Ulosi wa Danieli, tsa. 149
11 Ine ndikuitana mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa,*+Ndikuitana munthu kuchokera kudziko lakutali kuti adzachite zolinga zanga.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita. Ndakonza kuti zimenezi zichitike komanso ndidzazichita.+
46:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2024, tsa. 30 Yesaya 2, ptsa. 102-103 Nsanja ya Olonda,8/15/1999, tsa. 14 Ulosi wa Danieli, tsa. 149