-
Yesaya 47:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Tenga mphero upere ufa.
Vula nsalu yako yophimba kumutu.
Vula chovala chako ndipo miyendo yako ionekere.
Uwoloke mitsinje.
-