Yesaya 47:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe mwana wamkazi wa Akasidi,+Khala pansi mwakachetechete ndipo ulowe mumdima.Anthu sadzakutchulanso kuti Dona* wa Maufumu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:5 Yesaya 2, tsa. 108
5 Iwe mwana wamkazi wa Akasidi,+Khala pansi mwakachetechete ndipo ulowe mumdima.Anthu sadzakutchulanso kuti Dona* wa Maufumu.+