Yesaya 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano imva izi, iwe amene umakonda zosangalatsa,+Amene umakhala motetezeka, iwe amene umanena mumtima mwako kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.+ Sindidzakhala wamasiye Ndipo ana anga sadzafa.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:8 Yesaya 2, ptsa. 110-112, 119
8 Tsopano imva izi, iwe amene umakonda zosangalatsa,+Amene umakhala motetezeka, iwe amene umanena mumtima mwako kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.+ Sindidzakhala wamasiye Ndipo ana anga sadzafa.”+