Yesaya 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma zinthu ziwiri izi zidzakugwera modzidzimutsa tsiku limodzi:+ Ana ako adzafa ndiponso udzakhala wamasiye. Zinthu zonsezi zidzakugwera ndithu,+Chifukwa* wachita zanyanga zochuluka komanso chifukwa cha zamatsenga zako zonse zamphamvu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:9 Yesaya 2, ptsa. 112, 119
9 Koma zinthu ziwiri izi zidzakugwera modzidzimutsa tsiku limodzi:+ Ana ako adzafa ndiponso udzakhala wamasiye. Zinthu zonsezi zidzakugwera ndithu,+Chifukwa* wachita zanyanga zochuluka komanso chifukwa cha zamatsenga zako zonse zamphamvu.+