Yesaya 47:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho pitiriza kuchita zanyanga komanso zamatsenga zako zambirimbirizo,+Zimene wazivutikira kuyambira uli mwana. Mwina zingakuthandize,Mwina zichititsa kuti anthu achite mantha. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:12 Yesaya 2, ptsa. 113-114
12 Choncho pitiriza kuchita zanyanga komanso zamatsenga zako zambirimbirizo,+Zimene wazivutikira kuyambira uli mwana. Mwina zingakuthandize,Mwina zichititsa kuti anthu achite mantha.