-
Yesaya 47:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Iwotu ali ngati mapesi.
Moto udzawawotcha.
Sangathe kudzipulumutsa ku mphamvu ya moto walawilawi.
Moto umenewu suli ngati moto wamakala woti anthu nʼkumawotha,
Si moto woti anthu nʼkuuyandikira.
-