Yesaya 48:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndinakuuziranitu kalekale zinthu zimene zidzachitike. Zinatuluka pakamwa panga,Ndipo ndinazichititsa kuti zidziwike.+ Mwadzidzidzi, ndinachita zimene ndinanena ndipo zinachitikadi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:3 Yesaya 2, ptsa. 123, 125
3 “Ndinakuuziranitu kalekale zinthu zimene zidzachitike. Zinatuluka pakamwa panga,Ndipo ndinazichititsa kuti zidziwike.+ Mwadzidzidzi, ndinachita zimene ndinanena ndipo zinachitikadi.+