Yesaya 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndinakuuzani kalekale. Zisanachitike nʼkomwe, ine ndinachititsa kuti muzimve,Kuti musanene kuti, ‘Fano langa ndi limene linachita zimenezi.Chifaniziro changa chosema komanso chifaniziro chachitsulo* nʼzimene zinalamula zimenezi.’ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:5 Yesaya 2, ptsa. 123-124
5 Ine ndinakuuzani kalekale. Zisanachitike nʼkomwe, ine ndinachititsa kuti muzimve,Kuti musanene kuti, ‘Fano langa ndi limene linachita zimenezi.Chifaniziro changa chosema komanso chifaniziro chachitsulo* nʼzimene zinalamula zimenezi.’