Yesaya 48:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ndidzabweza mkwiyo wanga chifukwa cha dzina langa.+Chifukwa cha ulemerero wanga, ine ndidzadziletsaNdipo sindidzakuwonongani.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:9 Yesaya 2, ptsa. 126, 133
9 Koma ndidzabweza mkwiyo wanga chifukwa cha dzina langa.+Chifukwa cha ulemerero wanga, ine ndidzadziletsaNdipo sindidzakuwonongani.+