Yesaya 48:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndithu, ndidzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa,+Chifukwa sindingalole kuti dzina langa liipitsidwe.+ Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyense.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:11 Yesaya 2, ptsa. 126-127
11 Ndithu, ndidzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa,+Chifukwa sindingalole kuti dzina langa liipitsidwe.+ Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyense.*