Yesaya 48:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndimvere iwe Yakobo, iwe Isiraeli amene ndinakuitana. Ine sindinasinthe.+ Ine ndine woyamba. Ndinenso womaliza.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:12 Yesaya 2, ptsa. 129-130
12 Ndimvere iwe Yakobo, iwe Isiraeli amene ndinakuitana. Ine sindinasinthe.+ Ine ndine woyamba. Ndinenso womaliza.+