Yesaya 48:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Dzanja langa linayala maziko a dziko lapansi,+Ndipo dzanja langa lamanja linatambasula kumwamba.+ Ndikaitana zinthu zimenezi, zimaimirira limodzi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:13 Yesaya 2, ptsa. 129-130
13 Dzanja langa linayala maziko a dziko lapansi,+Ndipo dzanja langa lamanja linatambasula kumwamba.+ Ndikaitana zinthu zimenezi, zimaimirira limodzi.