Yesaya 49:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndimvereni zilumba inu,Ndipo mvetserani, inu mitundu yakutali.+ Yehova anandiitana ndisanabadwe.*+ Kuyambira nthawi imene ndinali mʼmimba mwa mayi anga, anatchula dzina langa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:1 Yesaya 2, tsa. 137
49 Ndimvereni zilumba inu,Ndipo mvetserani, inu mitundu yakutali.+ Yehova anandiitana ndisanabadwe.*+ Kuyambira nthawi imene ndinali mʼmimba mwa mayi anga, anatchula dzina langa.