Yesaya 49:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachititsa kuti mʼkamwa mwanga mukhale ngati lupanga lakuthwa.Wandibisa mumthunzi wa dzanja lake.+ Anandisandutsa muvi wonola bwino.Anandibisa mʼkachikwama kake koikamo mivi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:2 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, tsa. 15 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 282 Yesaya 2, ptsa. 137-138, 151
2 Iye anachititsa kuti mʼkamwa mwanga mukhale ngati lupanga lakuthwa.Wandibisa mumthunzi wa dzanja lake.+ Anandisandutsa muvi wonola bwino.Anandibisa mʼkachikwama kake koikamo mivi.
49:2 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, tsa. 15 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 282 Yesaya 2, ptsa. 137-138, 151