Yesaya 49:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuti ndiuze akaidi kuti, ‘Tulukani!’+ Ndiponso amene ali mumdima+ kuti, ‘Bwerani poyera kuti anthu akuoneni!’ Iwo adzadya msipu mʼmphepete mwa msewu,Ndipo mʼmphepete mwa njira zonse zimene zimadutsidwadutsidwa* mudzakhala malo awo odyeramo msipu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:9 Yesaya 2, tsa. 144
9 Kuti ndiuze akaidi kuti, ‘Tulukani!’+ Ndiponso amene ali mumdima+ kuti, ‘Bwerani poyera kuti anthu akuoneni!’ Iwo adzadya msipu mʼmphepete mwa msewu,Ndipo mʼmphepete mwa njira zonse zimene zimadutsidwadutsidwa* mudzakhala malo awo odyeramo msipu.