Yesaya 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sadzakhala ndi njala ndipo sadzamva ludzu,+Komanso sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Chifukwa amene amawachitira chifundo adzawatsogolera+Ndipo adzapita nawo kumene kuli akasupe amadzi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:10 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 127 Yesaya 2, tsa. 144
10 Iwo sadzakhala ndi njala ndipo sadzamva ludzu,+Komanso sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Chifukwa amene amawachitira chifundo adzawatsogolera+Ndipo adzapita nawo kumene kuli akasupe amadzi.+