Yesaya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+ Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:13 Yesaya 2, ptsa. 145-146
13 Fuulani mosangalala kumwamba inu ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule mosangalala.+ Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+Ndipo wachitira chifundo anthu ake ovutika.+