Yesaya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene amanena kuti ndine wolungama ali pafupi. Ndi ndani angandiimbe* mlandu?+ Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu. Kodi ndi ndani amene akufuna kundiimba mlandu? Abwere pafupi ndi ine. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 50:8 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 22 Yesaya 2, ptsa. 161-163
8 Amene amanena kuti ndine wolungama ali pafupi. Ndi ndani angandiimbe* mlandu?+ Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu. Kodi ndi ndani amene akufuna kundiimba mlandu? Abwere pafupi ndi ine.