-
Yesaya 50:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ndi ndani amene amayenda mumdima wandiweyani, popanda kuwala kulikonse?
Iye akhulupirire dzina la Yehova ndipo adalire Mulungu wake.
-