-
Yesaya 50:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 “Inu nonse amene mukuyatsa moto,
Amene mukuchititsa kuti uzithetheka,
Yendani mʼkuwala kwa moto wanuwo,
Pakati pa moto umene ukuthethekawo.
Izi ndi zimene mudzalandire kuchokera mʼdzanja langa:
Mudzagona pansi mukumva ululu woopsa.”
-