Yesaya 51:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimvereni, inu anthu amene mumadziwa chilungamo,Inu anthu amene chilamulo changa chili* mumtima mwanu.+ Musachite mantha ndi mawu otonza amene anthu akunenaNdipo musaope chifukwa cha mawu awo onyoza. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:7 Yesaya 2, ptsa. 171-172
7 Ndimvereni, inu anthu amene mumadziwa chilungamo,Inu anthu amene chilamulo changa chili* mumtima mwanu.+ Musachite mantha ndi mawu otonza amene anthu akunenaNdipo musaope chifukwa cha mawu awo onyoza.