Yesaya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu owomboledwa a Yehova adzabwerera.+ Adzabwera ku Ziyoni akufuula mosangalala,+Ndipo pamutu pawo padzakhala chisangalalo mpaka kalekale.+ Iwo adzapeza chisangalalo ndi chimwemwe,Ndipo chisoni komanso kulira zidzachoka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:11 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 303 Yesaya 2, ptsa. 173-174
11 Anthu owomboledwa a Yehova adzabwerera.+ Adzabwera ku Ziyoni akufuula mosangalala,+Ndipo pamutu pawo padzakhala chisangalalo mpaka kalekale.+ Iwo adzapeza chisangalalo ndi chimwemwe,Ndipo chisoni komanso kulira zidzachoka.+