Yesaya 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthoza.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani ukuopa munthu woti adzafa+Ndiponso mwana wa munthu amene adzanyale ngati udzu wobiriwira? Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:12 Yesaya 2, tsa. 174
12 “Ineyo ndi amene ndikukutonthoza.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani ukuopa munthu woti adzafa+Ndiponso mwana wa munthu amene adzanyale ngati udzu wobiriwira?