-
Yesaya 51:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Nʼchifukwa chiyani ukuiwala Yehova amene anakupanga,+
Amene anatambasula kumwamba+ ndi kuyala maziko a dziko lapansi?
Ndipo tsiku lonse unkangokhalira kuopa mkwiyo wa amene amakupondereza,
Ngati kuti ali ndi mphamvu zoti akanatha kukuwononga.
Kodi tsopano mkwiyo wa amene ankakupondereza uja uli kuti?
-