Yesaya 51:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzaika mawu anga mʼkamwa mwako,Ndipo ndidzakuphimba ndi mthunzi wa dzanja langa,+Kuti ndikhazikitse kumwamba komanso kuyala maziko a dziko lapansi+Ndiponso kuti ndiuze Ziyoni kuti, ‘Ndinu anthu anga.’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:16 Yesaya 2, ptsa. 175-176
16 Ndidzaika mawu anga mʼkamwa mwako,Ndipo ndidzakuphimba ndi mthunzi wa dzanja langa,+Kuti ndikhazikitse kumwamba komanso kuyala maziko a dziko lapansi+Ndiponso kuti ndiuze Ziyoni kuti, ‘Ndinu anthu anga.’+