Yesaya 51:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzuka! Dzuka! Imirira iwe Yerusalemu,+Iwe amene wamwa zinthu zamʼkapu ya mkwiyo wa Yehova kuchokera mʼdzanja lake. Iweyo wamwa zimene zili mʼchipanda,Wagugudiza kapu yochititsa kuti munthu aziyenda dzandidzandi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:17 Yesaya 2, tsa. 176
17 Dzuka! Dzuka! Imirira iwe Yerusalemu,+Iwe amene wamwa zinthu zamʼkapu ya mkwiyo wa Yehova kuchokera mʼdzanja lake. Iweyo wamwa zimene zili mʼchipanda,Wagugudiza kapu yochititsa kuti munthu aziyenda dzandidzandi.+