-
Yesaya 51:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Pa ana onse amene iye anabereka, palibe ndi mmodzi yemwe woti amutsogolere,
Ndipo pa ana onse amene iye analera, palibe ndi mmodzi yemwe amene wagwira dzanja lake.
-