Yesaya 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zinthu ziwiri izi zakugwera. Ndi ndani amene akumvere chisoni? Kuwonongedwa ndi kusakazidwa, njala ndi lupanga!+ Kodi ndi ndani amene akutonthoze?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:19 Yesaya 2, ptsa. 176-179
19 Zinthu ziwiri izi zakugwera. Ndi ndani amene akumvere chisoni? Kuwonongedwa ndi kusakazidwa, njala ndi lupanga!+ Kodi ndi ndani amene akutonthoze?+