Yesaya 51:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzaika kapu imeneyi mʼmanja mwa amene akukuvutitsa,+Amene amakuuza kuti, ‘Werama kuti tiyende pamsana pako.’ Choncho unachititsa kuti msana wako ukhale ngati malo oti azipondapo,Ngati msewu woti azidutsamo.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:23 Yesaya 2, tsa. 179
23 Ndidzaika kapu imeneyi mʼmanja mwa amene akukuvutitsa,+Amene amakuuza kuti, ‘Werama kuti tiyende pamsana pako.’ Choncho unachititsa kuti msana wako ukhale ngati malo oti azipondapo,Ngati msewu woti azidutsamo.”