-
Yesaya 52:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Tamvera! Alonda ako akufuula.
Onse akufuula pamodzi mosangalala,
Chifukwa akuona bwinobwino pamene Yehova akusonkhanitsanso anthu okhala mu Ziyoni.
-