Yesaya 52:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova waika poyera dzanja lake loyera kuti mitundu yonse ione.+Ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzaona zimene Mulungu wathu wachita potipulumutsa.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:10 Yesaya 2, ptsa. 190-191 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, tsa. 12
10 Yehova waika poyera dzanja lake loyera kuti mitundu yonse ione.+Ndipo malekezero onse a dziko lapansi adzaona zimene Mulungu wathu wachita potipulumutsa.*+