Yesaya 52:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa simudzachoka mopanikizika,Ndipo simudzafunika kuthawa,Popeza Yehova azidzayenda patsogolo panu,+Ndipo Mulungu wa Isiraeli azidzalondera kumbuyo kwanu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:12 Yesaya 2, ptsa. 191, 193
12 Chifukwa simudzachoka mopanikizika,Ndipo simudzafunika kuthawa,Popeza Yehova azidzayenda patsogolo panu,+Ndipo Mulungu wa Isiraeli azidzalondera kumbuyo kwanu.+