Yesaya 54:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 “Fuula mosangalala iwe mkazi amene sunaberekepo mwana.+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ sangalala ndipo ufuule mosangalala.+Chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiriKuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”*+ akutero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:1 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, tsa. 118/1/1995, tsa. 117/1/1989, tsa. 21 Yesaya 2, ptsa. 216-221
54 “Fuula mosangalala iwe mkazi amene sunaberekepo mwana.+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ sangalala ndipo ufuule mosangalala.+Chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiriKuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”*+ akutero Yehova.