Yesaya 54:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Udzakhazikika molimba mʼchilungamo.+ Palibe amene adzakupondereze,+Sudzaopa kanthu ndipo palibe chimene chidzakuchititse mantha,Chifukwa palibe chilichonse choopsa chimene chidzakuyandikire.+
14 Udzakhazikika molimba mʼchilungamo.+ Palibe amene adzakupondereze,+Sudzaopa kanthu ndipo palibe chimene chidzakuchititse mantha,Chifukwa palibe chilichonse choopsa chimene chidzakuyandikire.+