Yesaya 55:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Ine ndinamuchititsa kuti akhale mboni+ ku mitundu ya anthu,Ndiponso kuti akhale mtsogoleri+ ndi wolamulira+ wa mitundu ya anthu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:4 Gulu, ptsa. 13-14 Nsanja ya Olonda,4/1/2007, tsa. 27 Yesaya 2, ptsa. 238-242
4 Taonani! Ine ndinamuchititsa kuti akhale mboni+ ku mitundu ya anthu,Ndiponso kuti akhale mtsogoleri+ ndi wolamulira+ wa mitundu ya anthu.