Yesaya 55:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe udzaitana mtundu umene sukuudziwa,Ndipo anthu a mtundu umene sukukudziwa adzathamangira kwa iweChifukwa cha Yehova Mulungu wako,+ Woyera wa Isiraeli,Komanso chifukwa chakuti adzakupatsa ulemerero.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:5 Yesaya 2, ptsa. 241-242
5 Iwe udzaitana mtundu umene sukuudziwa,Ndipo anthu a mtundu umene sukukudziwa adzathamangira kwa iweChifukwa cha Yehova Mulungu wako,+ Woyera wa Isiraeli,Komanso chifukwa chakuti adzakupatsa ulemerero.+