Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:7 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 57 Yesaya 2, tsa. 243 Nsanja ya Olonda,9/15/1992, tsa. 8
7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+
55:7 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 57 Yesaya 2, tsa. 243 Nsanja ya Olonda,9/15/1992, tsa. 8