Yesaya 55:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Chifukwa mofanana ndi kumwamba kumene kuli pamwamba kuposa dziko lapansi,Njira zanganso nʼzapamwamba kuposa njira zanuNdipo maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:9 Yesaya 2, ptsa. 243-244
9 “Chifukwa mofanana ndi kumwamba kumene kuli pamwamba kuposa dziko lapansi,Njira zanganso nʼzapamwamba kuposa njira zanuNdipo maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+