Yesaya 55:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+Koma adzachitadi chilichonse chimene ine ndikufuna,+Ndipo zimene ndinawatumizira kuti achite zidzachitikadi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:11 Yandikirani, ptsa. 283-284 Galamukani!,12/2008, ptsa. 6-7 Nsanja ya Olonda,8/15/2006, tsa. 66/1/2006, ptsa. 22-23 Yesaya 2, ptsa. 244-246
11 Ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+Koma adzachitadi chilichonse chimene ine ndikufuna,+Ndipo zimene ndinawatumizira kuti achite zidzachitikadi.
55:11 Yandikirani, ptsa. 283-284 Galamukani!,12/2008, ptsa. 6-7 Nsanja ya Olonda,8/15/2006, tsa. 66/1/2006, ptsa. 22-23 Yesaya 2, ptsa. 244-246