Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa mudzapita mukusangalala,+Ndipo adzakubweretsani kwanu mwamtendere.+ Mukadzafika, mapiri ndi zitunda zidzafuula mosangalala,+Ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba mʼmanja.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:12 Yesaya 2, ptsa. 245-246
12 Chifukwa mudzapita mukusangalala,+Ndipo adzakubweretsani kwanu mwamtendere.+ Mukadzafika, mapiri ndi zitunda zidzafuula mosangalala,+Ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba mʼmanja.+