Yesaya 55:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mʼmalo mwa chitsamba chaminga padzamera mtengo wa junipa.*+Mʼmalo mwa chomera choyabwa padzamera mtengo wa mchisu. Zinthu zimenezi zidzachititsa kuti Yehova atchuke,*+Ndipo zidzakhala chizindikiro chamuyaya chimene sichidzawonongeka.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:13 Yesaya 2, ptsa. 245-246
13 Mʼmalo mwa chitsamba chaminga padzamera mtengo wa junipa.*+Mʼmalo mwa chomera choyabwa padzamera mtengo wa mchisu. Zinthu zimenezi zidzachititsa kuti Yehova atchuke,*+Ndipo zidzakhala chizindikiro chamuyaya chimene sichidzawonongeka.”