Yesaya 56:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Yehova wanena kuti: “Tsatirani chilungamo+ ndipo chitani zolungama,Chifukwa chipulumutso changa chatsala pangʼono kubweraNdipo chilungamo changa chidzaonekera.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:1 Yesaya 2, tsa. 248
56 Yehova wanena kuti: “Tsatirani chilungamo+ ndipo chitani zolungama,Chifukwa chipulumutso changa chatsala pangʼono kubweraNdipo chilungamo changa chidzaonekera.+