Yesaya 56:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo palibe amene akudziwa zimene zichitike.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu ndipo satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:10 Yesaya 2, ptsa. 258-260
10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo palibe amene akudziwa zimene zichitike.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu ndipo satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo.