Yesaya 57:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Gawo lako lili pamodzi ndi miyala yosalala yamʼchigwa.*+ Inde, gawo lako ndi limeneli. Ndipo umapereka nsembe zachakumwa, ndiponso mphatso kwa zinthu zimenezi.+ Kodi ine ndikhutire* ndi zinthu zimenezi? Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:6 Yesaya 2, ptsa. 264-265
6 Gawo lako lili pamodzi ndi miyala yosalala yamʼchigwa.*+ Inde, gawo lako ndi limeneli. Ndipo umapereka nsembe zachakumwa, ndiponso mphatso kwa zinthu zimenezi.+ Kodi ine ndikhutire* ndi zinthu zimenezi?