-
Yesaya 57:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Unaika chizindikiro chachikumbutso chako kuseri kwa chitseko ndi kuseri kwa felemu.
Iwe unandisiya ndipo unavula.
Unakwera mtunda nʼkukulitsa bedi lako.
Ndipo unachita nawo pangano.
-