Yesaya 57:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Watopa chifukwa chotsatira njira zako zambiri,Koma sunanene kuti, ‘Nʼzopanda phindu!’ Unapeza mphamvu zina. Nʼchifukwa chake sunafooke.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:10 Yesaya 2, tsa. 268
10 Watopa chifukwa chotsatira njira zako zambiri,Koma sunanene kuti, ‘Nʼzopanda phindu!’ Unapeza mphamvu zina. Nʼchifukwa chake sunafooke.*