Yesaya 57:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi unkaopa komanso kuchita mantha ndi ndaniKuti uyambe kunama?+ Ine sunandikumbukire.+ Palibe chimene unaganizira mumtima mwako.+ Kodi si paja ine ndinakhala chete ndipo sindinachitepo kanthu pa zochita zako?+ Choncho iweyo sunkandiopa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 57:11 Yesaya 2, tsa. 269
11 Kodi unkaopa komanso kuchita mantha ndi ndaniKuti uyambe kunama?+ Ine sunandikumbukire.+ Palibe chimene unaganizira mumtima mwako.+ Kodi si paja ine ndinakhala chete ndipo sindinachitepo kanthu pa zochita zako?+ Choncho iweyo sunkandiopa.